-
Yesaya 65:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Atumiki anga adzafuula mosangalala chifukwa chokhala ndi chimwemwe mumtima,
Koma inu mudzalira chifukwa chopwetekedwa mtima
Ndipo mudzalira mofuula chifukwa chosweka mtima.
-