Yesaya 65:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Moti aliyense wofuna kudalitsidwa padziko lapansiAdzadalitsidwa ndi Mulungu amene amanena zoona,*Ndipo aliyense wochita lumbiro padziko lapansiAdzalumbira pa Mulungu amene amanena zoona.*+ Chifukwa mavuto akale adzaiwalikaAdzabisidwa kuti ndisawaonenso.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 65:16 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),11/2023, tsa. 2 Yesaya 2, ptsa. 380-381
16 Moti aliyense wofuna kudalitsidwa padziko lapansiAdzadalitsidwa ndi Mulungu amene amanena zoona,*Ndipo aliyense wochita lumbiro padziko lapansiAdzalumbira pa Mulungu amene amanena zoona.*+ Chifukwa mavuto akale adzaiwalikaAdzabisidwa kuti ndisawaonenso.+