-
Yesaya 66:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mumzinda mukumveka phokoso lachipwirikiti, phokoso lochokera kukachisi.
Limeneli ndi phokoso losonyeza kuti Yehova akubwezera adani ake chilango chowayenerera.
-