-
Yesaya 66:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndi ndani anamvapo zinthu ngati zimenezi?
Ndi ndani anaonapo zinthu zoterezi?
Kodi dziko lingabadwe tsiku limodzi?
Kapena kodi mtundu wa anthu ungabadwe nthawi imodzi?
Koma Ziyoni atangoyamba kumva zowawa za pobereka, anabereka ana aamuna.
-