-
Yesaya 66:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa mudzayamwa bere lake lotonthoza ndipo mudzakhuta kwambiri,
Komanso mudzamwa mkaka wake mokwanira ndipo mudzasangalala kwambiri ndi ulemerero wake.
-