Yesaya 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndikumupatsa mtendere ngati mtsinje+Komanso ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira.+ Inu mudzayamwa komanso adzakunyamulani mʼmanja,Ndipo adzakudumphitsani pamiyendo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:12 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),9/2018, ptsa. 13-14 Yesaya 2, ptsa. 400-401
12 Chifukwa Yehova wanena kuti: “Ndikumupatsa mtendere ngati mtsinje+Komanso ulemerero wa mitundu ya anthu ngati mtsinje wosefukira.+ Inu mudzayamwa komanso adzakunyamulani mʼmanja,Ndipo adzakudumphitsani pamiyendo.