Yesaya 66:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chifukwa Yehova adzabwera ngati moto,+Ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho,+Kuti adzawabwezere atakwiya kwambiri,Ndiponso kuti adzawadzudzule ndi malawi a moto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:15 Yesaya 2, ptsa. 404-405
15 “Chifukwa Yehova adzabwera ngati moto,+Ndipo magaleta ake ali ngati mphepo yamkuntho,+Kuti adzawabwezere atakwiya kwambiri,Ndiponso kuti adzawadzudzule ndi malawi a moto.+