Yesaya 66:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:17 Yesaya 2, tsa. 405
17 Anthu amene akudzipatula nʼkudziyeretsa potsatira fano limene lili pakati pa mundawo,*+ amene akudya nyama ya nkhumba,+ zinthu zonyansa komanso mbewa,+ onsewo adzathera limodzi,” akutero Yehova.