Yesaya 66:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Kuyambira tsiku limene mwezi watsopano waoneka mpaka tsiku limene mwezi wina watsopano udzaoneke ndiponso sabata lililonse,Anthu onse adzabwera kudzagwada* pamaso panga,”+ akutero Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:23 Nsanja ya Olonda,11/1/2006, tsa. 314/15/2000, ptsa. 14-15 Yesaya 2, tsa. 412
23 “Kuyambira tsiku limene mwezi watsopano waoneka mpaka tsiku limene mwezi wina watsopano udzaoneke ndiponso sabata lililonse,Anthu onse adzabwera kudzagwada* pamaso panga,”+ akutero Yehova.