Yeremiya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ndisanakuumbe mʼmimba, ndinkakudziwa,*+Ndipo usanabadwe,* ndinakusankha* kuti ugwire ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:5 Yeremiya, ptsa. 6-7 Nsanja ya Olonda,4/1/1988, tsa. 10
5 “Ndisanakuumbe mʼmimba, ndinkakudziwa,*+Ndipo usanabadwe,* ndinakusankha* kuti ugwire ntchito yopatulika.+ Ndinakusankha kuti ukhale mneneri ku mitundu ya anthu.”