Yeremiya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma ine ndinati: “Ayi musatero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ine sinditha kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Nsanja ya Olonda,3/15/2011, tsa. 294/1/1988, tsa. 10 Yeremiya, tsa. 7
6 Koma ine ndinati: “Ayi musatero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Ine sinditha kulankhula+ chifukwa ndine mwana.”+