Yeremiya 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehova anatambasula dzanja lake nʼkukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga mʼkamwa mwako.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Yeremiya, ptsa. 33-35
9 Kenako Yehova anatambasula dzanja lake nʼkukhudza pakamwa panga.+ Ndiyeno Yehova anandiuza kuti: “Ndaika mawu anga mʼkamwa mwako.+