Yeremiya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa anthu anga chifukwa cha zoipa zawo zonse,Chifukwa iwo andisiya+Ndipo akupereka nsembe zofukiza kwa milungu ina+Komanso akugwadira ntchito za manja awo.’+
16 Ndipo ine ndidzapereka zigamulo zanga pa anthu anga chifukwa cha zoipa zawo zonse,Chifukwa iwo andisiya+Ndipo akupereka nsembe zofukiza kwa milungu ina+Komanso akugwadira ntchito za manja awo.’+