Yeremiya 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa lero ndakupanga kuti ukhale mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,Chipilala cha chitsulo ndi makoma akopa* kuti dziko lonseli lisakugonjetse.+Kuti mafumu a Yuda, akalonga ake,Ansembe ake ndi anthu amʼdzikoli asakugonjetse.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Nsanja ya Olonda,3/15/2011, tsa. 32
18 Chifukwa lero ndakupanga kuti ukhale mzinda wokhala ndi mpanda wolimba kwambiri,Chipilala cha chitsulo ndi makoma akopa* kuti dziko lonseli lisakugonjetse.+Kuti mafumu a Yuda, akalonga ake,Ansembe ake ndi anthu amʼdzikoli asakugonjetse.+