Yeremiya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira pa zokolola zake.”’ ‘Aliyense wofuna kumumeza akanakhala ndi mlandu. Tsoka likanamugwera,’ akutero Yehova.”+
3 Isiraeli anali wopatulika kwa Yehova,+ ndipo anali zipatso zoyambirira pa zokolola zake.”’ ‘Aliyense wofuna kumumeza akanakhala ndi mlandu. Tsoka likanamugwera,’ akutero Yehova.”+