Yeremiya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ansembe sanafunse kuti, ‘Ali kuti Yehova?’+ Amene ankaphunzitsa Chilamulo sankandidziwa,Abusa anandipandukira,+Aneneri ankalosera mʼdzina la Baala,+Ndipo ankatsatira milungu yopanda phindu.
8 Ansembe sanafunse kuti, ‘Ali kuti Yehova?’+ Amene ankaphunzitsa Chilamulo sankandidziwa,Abusa anandipandukira,+Aneneri ankalosera mʼdzina la Baala,+Ndipo ankatsatira milungu yopanda phindu.