Yeremiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ‘Koma wolokerani kuzilumba za ku Kitimu+ kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwinoNʼkuona ngati zoterezi zinayamba zachitikapo kumeneko. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:10 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
10 ‘Koma wolokerani kuzilumba za ku Kitimu+ kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwinoNʼkuona ngati zoterezi zinayamba zachitikapo kumeneko.