-
Yeremiya 2:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 ‘Kodi Isiraeli ndi mtumiki wanga kapena ndi kapolo wobadwira mʼnyumba mwanga?
Nanga nʼchifukwa chiyani anthu anamugwira nʼkupita naye kudziko lina?
-