Yeremiya 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiye nʼchifukwa chiyani ukufuna kuyenda mʼnjira ya ku Iguputo+Kuti ukamwe madzi amumtsinje wa Sihori?* Nʼchifukwa chiyani ukufuna kuyenda mʼnjira yopita kudziko la Asuri+Kuti ukamwe madzi amumtsinje wa Firate?
18 Ndiye nʼchifukwa chiyani ukufuna kuyenda mʼnjira ya ku Iguputo+Kuti ukamwe madzi amumtsinje wa Sihori?* Nʼchifukwa chiyani ukufuna kuyenda mʼnjira yopita kudziko la Asuri+Kuti ukamwe madzi amumtsinje wa Firate?