Yeremiya 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ine ndinakudzala ngati mtengo wa mpesa wofiira,+ wabwino kwambiri umene unamera kuchokera ku mbewu yabwino kwambiri.Ndiye wandisinthira bwanji nʼkukhala mphukira zachabechabe za mtengo wa mpesa wachilendo?’+
21 Ine ndinakudzala ngati mtengo wa mpesa wofiira,+ wabwino kwambiri umene unamera kuchokera ku mbewu yabwino kwambiri.Ndiye wandisinthira bwanji nʼkukhala mphukira zachabechabe za mtengo wa mpesa wachilendo?’+