-
Yeremiya 2:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Uli ngati bulu wamʼtchire amene anazolowera kukhala mʼchipululu,
Amene amanunkhiza pofunafuna amuna chifukwa cha chilakolako chake champhamvu.
Ndi ndani amene angamubweze nthawi yoti akweredwe ikakwana?
Abulu amphongo amene akumufunafuna sadzavutika kuti amupeze.
Nyengo yoti* akweredwe ikakwana adzamupeza.
-