Yeremiya 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Iwo amauza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ Ndipo mwala amauuza kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Koma ine andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti,‘Bwerani mudzatipulumutse!’+
27 Iwo amauza mtengo kuti, ‘Ndinu bambo anga,’+ Ndipo mwala amauuza kuti, ‘Ndinu amene munandibereka.’ Koma ine andifulatira ndipo sanandisonyeze nkhope yawo.+ Koma tsoka likadzawagwera adzanena kuti,‘Bwerani mudzatipulumutse!’+