Yeremiya 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kodi milungu yako imene unapanga ija ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka,Chifukwa iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+
28 Kodi milungu yako imene unapanga ija ili kuti?+ Imeneyo ibwere kwa iwe ngati ingathe kukupulumutsa pa nthawi ya tsoka,Chifukwa iwe Yuda, milungu yako yachuluka mofanana ndi mizinda yako.+