Yeremiya 2:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndalanga ana anu aamuna koma sizinathandize.+ Iwo sanalole kulandira chilango.*+Lupanga lanu linapha aneneri anu,+Ngati mkango wolusa.
30 Ndalanga ana anu aamuna koma sizinathandize.+ Iwo sanalole kulandira chilango.*+Lupanga lanu linapha aneneri anu,+Ngati mkango wolusa.