Yeremiya 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu anthu anga, ganizirani mawu a Yehova. “Kodi ine ndakhala ngati chipululu kwa IsiraeliKapena ngati dziko lamdima wandiweyani? Nʼchifukwa chiyani anthu angawa anena kuti, ‘Tikungoyendayenda mmene tikufunira. Sitibweranso kwa inuʼ?+
31 Inu anthu anga, ganizirani mawu a Yehova. “Kodi ine ndakhala ngati chipululu kwa IsiraeliKapena ngati dziko lamdima wandiweyani? Nʼchifukwa chiyani anthu angawa anena kuti, ‘Tikungoyendayenda mmene tikufunira. Sitibweranso kwa inuʼ?+