Yeremiya 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kodi namwali angaiwale zinthu zake zodzikongoletsera?Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wapachifuwa?* Komatu anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+
32 Kodi namwali angaiwale zinthu zake zodzikongoletsera?Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wapachifuwa?* Komatu anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+