Yeremiya 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ngakhale zovala zako zathimbirira ndi magazi a anthu osauka omwe ndi osalakwa,+Ngakhale kuti anthuwo sindinawapeze akuthyola nyumba kuti abe,Ndaona kuti magazi awo ali pazovala zako zonse.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:34 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 14
34 Ngakhale zovala zako zathimbirira ndi magazi a anthu osauka omwe ndi osalakwa,+Ngakhale kuti anthuwo sindinawapeze akuthyola nyumba kuti abe,Ndaona kuti magazi awo ali pazovala zako zonse.+