Yeremiya 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Pa chifukwa chimenechi, udzayenda manja ako ali kumutu,+Chifukwa Yehova wakana amene umawadaliraNdipo iwo sadzakuthandiza kuti zinthu zikuyendere bwino.”
37 Pa chifukwa chimenechi, udzayenda manja ako ali kumutu,+Chifukwa Yehova wakana amene umawadaliraNdipo iwo sadzakuthandiza kuti zinthu zikuyendere bwino.”