Yeremiya 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yangʼana pamwamba pa mapiri ndipo uone. Kodi ndi pamalo ati pamene amuna sanakugonerepo? Unkakhala mʼmbali mwa njira nʼkumawadikiriraNgati munthu wongoyendayenda* mʼchipululu. Ukupitiriza kuipitsa dzikoliNdi uhule wako komanso kuipa kwako.+
2 Yangʼana pamwamba pa mapiri ndipo uone. Kodi ndi pamalo ati pamene amuna sanakugonerepo? Unkakhala mʼmbali mwa njira nʼkumawadikiriraNgati munthu wongoyendayenda* mʼchipululu. Ukupitiriza kuipitsa dzikoliNdi uhule wako komanso kuipa kwako.+