Yeremiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku a Mfumu Yosiya,+ Yehova anandiuza kuti: “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita? Akupita kuphiri lililonse lalitali ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira kuti akachite uhule kumeneko.+
6 Mʼmasiku a Mfumu Yosiya,+ Yehova anandiuza kuti: “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita? Akupita kuphiri lililonse lalitali ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira kuti akachite uhule kumeneko.+