Yeremiya 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale kuti anachita zonsezi, ine ndinamupempha mobwerezabwereza kuti abwerere kwa ine,+ koma iye sanabwerere. Ndipo Yuda ankangoyangʼana zimene mchemwali wake wachinyengoyo ankachita.+
7 Ngakhale kuti anachita zonsezi, ine ndinamupempha mobwerezabwereza kuti abwerere kwa ine,+ koma iye sanabwerere. Ndipo Yuda ankangoyangʼana zimene mchemwali wake wachinyengoyo ankachita.+