-
Yeremiya 3:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Ngakhale kuti anachita zonsezi, mchemwali wake Yuda amene ndi wachinyengo sanabwerere kwa ine ndi mtima wake wonse, koma anangobwerera mwachiphamaso,’ akutero Yehova.”
-