Yeremiya 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto:+ ‘Yehova wanena kuti:+ “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyangʼana mokwiya+ chifukwa ndine wokhulupirika,” akutero Yehova. “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Yeremiya, ptsa. 150-152 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 9
12 Pita, ndipo ukalengeze mawu awa kumpoto:+ ‘Yehova wanena kuti:+ “Bwerera Isiraeli wopanduka iwe. Sindidzakuyangʼana mokwiya+ chifukwa ndine wokhulupirika,” akutero Yehova. “Sindidzakhala wokwiya mpaka kalekale.