Yeremiya 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma vomerezani kuti ndinu olakwa chifukwa mwapandukira Yehova Mulungu wanu. Munapitiriza kuchita chiwerewere ndi anthu achilendo* pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira. Koma simunamvere mawu anga,” akutero Yehova.’”
13 Koma vomerezani kuti ndinu olakwa chifukwa mwapandukira Yehova Mulungu wanu. Munapitiriza kuchita chiwerewere ndi anthu achilendo* pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira. Koma simunamvere mawu anga,” akutero Yehova.’”