Yeremiya 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzakupatsani abusa amene amachita zinthu zogwirizana ndi zofuna zanga+ ndipo adzakuthandizani kuti mudziwe zinthu zambiri ndiponso kuti mukhale omvetsa zinthu. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:15 Yeremiya, ptsa. 129-130 Nsanja ya Olonda,3/15/1989, ptsa. 13-15
15 Ndidzakupatsani abusa amene amachita zinthu zogwirizana ndi zofuna zanga+ ndipo adzakuthandizani kuti mudziwe zinthu zambiri ndiponso kuti mukhale omvetsa zinthu.