Yeremiya 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Masiku amenewo Mudzaberekana ndipo mudzakhala ambiri mʼdzikoli,” akutero Yehova.+ “Iwo sadzanenanso kuti, ‘Likasa la pangano la Yehova!’ Sadzaliganiziranso mʼmitima yawo, kulikumbukira kapena kulilakalaka ndipo sadzapanganso likasa lina.
16 Masiku amenewo Mudzaberekana ndipo mudzakhala ambiri mʼdzikoli,” akutero Yehova.+ “Iwo sadzanenanso kuti, ‘Likasa la pangano la Yehova!’ Sadzaliganiziranso mʼmitima yawo, kulikumbukira kapena kulilakalaka ndipo sadzapanganso likasa lina.