Yeremiya 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa nthawi imeneyo mzinda wa Yerusalemu adzautchula kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsa pamodzi ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso khosi nʼkumatsatira mitima yawo yoipayo.
17 Pa nthawi imeneyo mzinda wa Yerusalemu adzautchula kuti mpando wachifumu wa Yehova.+ Ndipo mitundu yonse adzaisonkhanitsa pamodzi ku Yerusalemu kuti ikatamande dzina la Yehova+ kumeneko. Iwo sadzaumitsanso khosi nʼkumatsatira mitima yawo yoipayo.