Yeremiya 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼmasiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli.+ Onse pamodzi adzabwera kuchokera mʼdziko lakumpoto nʼkulowa mʼdziko limene ndinapereka kwa makolo anu kuti likhale cholowa chawo.+
18 Mʼmasiku amenewo nyumba ya Yuda idzayenda pamodzi ndi nyumba ya Isiraeli.+ Onse pamodzi adzabwera kuchokera mʼdziko lakumpoto nʼkulowa mʼdziko limene ndinapereka kwa makolo anu kuti likhale cholowa chawo.+