Yeremiya 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ‘Ndithudi, mofanana ndi mkazi amene amasiya mwamuna wake mwachinyengo, inunso a mʼnyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ akutero Yehova.”
20 ‘Ndithudi, mofanana ndi mkazi amene amasiya mwamuna wake mwachinyengo, inunso a mʼnyumba ya Isiraeli mwandichitira zachinyengo,’+ akutero Yehova.”