Yeremiya 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Bwererani, inu ana opanduka. Ndidzachiritsa mtima wanu wopandukawo.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu,Chifukwa inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:22 Yeremiya, ptsa. 71-72
22 “Bwererani, inu ana opanduka. Ndidzachiritsa mtima wanu wopandukawo.”+ “Ife tabwerera! Tabwera kwa inu,Chifukwa inu Yehova ndinu Mulungu wathu.+