Yeremiya 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndithudi, tinkangodzinamiza tokha pochitira milungu ina zikondwerero zaphokoso mʼzitunda ndi mʼmapiri.+ Kunena zoona chipulumutso cha Isiraeli chimachokera kwa Yehova Mulungu wathu.+
23 Ndithudi, tinkangodzinamiza tokha pochitira milungu ina zikondwerero zaphokoso mʼzitunda ndi mʼmapiri.+ Kunena zoona chipulumutso cha Isiraeli chimachokera kwa Yehova Mulungu wathu.+