Yeremiya 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma chinthu chochititsa manyazi chadya* zinthu zonse zimene makolo athu anazipeza movutikira kuyambira tili anyamata.+Chadya nkhosa zawo ndi ngʼombe zawo,Ana awo aamuna ndi ana awo aakazi.
24 Koma chinthu chochititsa manyazi chadya* zinthu zonse zimene makolo athu anazipeza movutikira kuyambira tili anyamata.+Chadya nkhosa zawo ndi ngʼombe zawo,Ana awo aamuna ndi ana awo aakazi.