Yeremiya 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tiyeni tigone pansi mwamanyazi,Ndipo manyazi athuwo atiphimbe,Chifukwa tachimwira Yehova Mulungu wathu,+Ifeyo pamodzi ndi makolo athu kuyambira tili achinyamata mpaka pano,+Ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu.”
25 Tiyeni tigone pansi mwamanyazi,Ndipo manyazi athuwo atiphimbe,Chifukwa tachimwira Yehova Mulungu wathu,+Ifeyo pamodzi ndi makolo athu kuyambira tili achinyamata mpaka pano,+Ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu.”