Yeremiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli,Ngati ungabwerere kwa ineNdipo ngati ungachotse mafano ako onyansa pamaso panga,Sudzakhalanso moyo wothawathawa.+
4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli,Ngati ungabwerere kwa ineNdipo ngati ungachotse mafano ako onyansa pamaso panga,Sudzakhalanso moyo wothawathawa.+