Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati ungalumbire,Mʼchoonadi komanso mwachilungamo kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo,’Ndiye kuti mitundu ya anthu idzapeza madalitso kudzera mwa iyeNdipo idzauza ena za iye monyadira.”+
2 Ndipo ngati ungalumbire,Mʼchoonadi komanso mwachilungamo kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo,’Ndiye kuti mitundu ya anthu idzapeza madalitso kudzera mwa iyeNdipo idzauza ena za iye monyadira.”+