Yeremiya 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chitani mdulidwe pamaso pa Yehova,Chitani mdulidwe wa mitima yanu,+Inu anthu a ku Yuda komanso anthu amene mukukhala mu Yerusalemu,Kuti mkwiyo wanga usayake ngati moto,Usayake popanda aliyense wowuzimitsa,Chifukwa cha zochita zanu zoipa.”+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:4 Nsanja ya Olonda,3/15/2013, ptsa. 9-103/15/2007, tsa. 9
4 Chitani mdulidwe pamaso pa Yehova,Chitani mdulidwe wa mitima yanu,+Inu anthu a ku Yuda komanso anthu amene mukukhala mu Yerusalemu,Kuti mkwiyo wanga usayake ngati moto,Usayake popanda aliyense wowuzimitsa,Chifukwa cha zochita zanu zoipa.”+