Yeremiya 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nenani zimenezi mu Yuda ndipo zilengezeni mu Yerusalemu. Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa mʼdziko lonse.+ Fuulani ndipo nenani kuti: “Sonkhanani pamodzi,Tiyeni tithawire mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
5 Nenani zimenezi mu Yuda ndipo zilengezeni mu Yerusalemu. Fuulani ndi kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa mʼdziko lonse.+ Fuulani ndipo nenani kuti: “Sonkhanani pamodzi,Tiyeni tithawire mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+