Yeremiya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni. Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,” Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.
6 Kwezani chizindikiro choloza njira ya ku Ziyoni. Thawirani kumalo otetezeka, musangoima,” Chifukwa ndikubweretsa tsoka kuchokera kumpoto,+ tsoka lalikulu kwambiri.