Yeremiya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawi imeneyo anthu awa komanso Yerusalemu adzauzidwa kuti: “Mphepo yotentha imene ikuchokera mʼmapiri opanda kanthu amʼchipululu,Idzaomba pamwana wamkazi wa anthu anga.Mphepo imeneyi sikubwera kuti idzauluze mankhusu* kapena kudzayeretsa tirigu.
11 Pa nthawi imeneyo anthu awa komanso Yerusalemu adzauzidwa kuti: “Mphepo yotentha imene ikuchokera mʼmapiri opanda kanthu amʼchipululu,Idzaomba pamwana wamkazi wa anthu anga.Mphepo imeneyi sikubwera kuti idzauluze mankhusu* kapena kudzayeretsa tirigu.