Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:28 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 109
28 Pachifukwa chimenechi dzikolo lidzalira,+Ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndasankha kuchita zimenezi,Ndipo sindidzasintha maganizo anga* kapena kulephera kuchita zimenezi.+